找歌词就来最浮云

《Hear Me》歌词

所属专辑: Makes a King 歌手: The Very Best 时长: 04:40
Hear Me

[00:04:40] CHICHEWA

[00:04:40] Siyani dumbo

[00:04:40] Siyani umbombo

[00:04:40] Tatopa nazo kodi simukudziwa kuti lija ndi kale?

[00:04:40] Siya umbanda

[00:04:40] Siya zauchigawenga

[00:04:40] Kodi watani iwe siukudziwa kuti kupha ndi sambi?

[00:04:40] Siyani dumbo

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Siya kaduka

[00:04:40] Siya zokonda kuba

[00:04:40] Siyani chinyengo kuyambila lero tiyeni tikonze tsogolo

[00:04:40] Siyani kugona

[00:04:40] Siya kugona tulo

[00:04:40] Kunja kwacha kodi simukuona kuti dzuwa latuluka?

[00:04:40] Siya kaduka

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Hear me now

[00:04:40] Dzaka makumi asanu

[00:04:40] Zatha kufika lero

[00:04:40] Mpaka lero umphawi

[00:04:40] Ukungophabe dziko

[00:04:40] Dzaka makumi asanu

[00:04:40] Zatha kufika lero

[00:04:40] Mpaka lero umphawi

[00:04:40] Ukungophabe dziko

您可能还喜欢歌手The Very Best的歌曲: