找歌词就来最浮云

《Yoshua Alikuti》歌词

所属专辑: Yoshua Alikuti (Single) 歌手: The Very Best 时长: 04:13
Yoshua Alikuti

[00:00:00] Yoshua Alikuti - The Very Best

[00:00:16] Ana a mulungu

[00:00:18] Aisiraeli azunzika m'chipululu

[00:00:25] Bambo Mose musatayilire

[00:00:29] Namalenga ati mulamulire

[00:00:33] Lero mwataya chipangano

[00:00:37] Kuyamba kupembedza makavalo

[00:00:42] Alikuti yoswayo

[00:00:46] Adzabwera liti

[00:00:48] Tifuna chipulumutso

[00:00:52] Wanyoza mtundu wanga

[00:00:56] Iwe walakwa

[00:00:57] Walakwa

[00:01:01] Waphetsa mtundu wanga

[00:01:05] Ndati walakwa

[00:01:06] Ndati walakwa

[00:01:08] Alikuti yosuayo

[00:01:12] Adzabwera liti

[00:01:14] Tifuna chipulumutso

[00:01:17] Sitifuna mose wina

[00:01:21] Wankhambakamwa

[00:01:22] Wodzatisocheretsa

[00:01:25] Alikuti yosuayo

[00:01:30] Adzabwera liti

[00:01:31] Tifuna chipulumutso

[00:01:34] Sitifuna mose wina

[00:01:38] Wankhambakamwa

[00:01:40] Wodzatisocheretsa

[00:01:44] Ulendo wochokera kwa iguputo

[00:01:49] Unali wautali

[00:01:52] Munatiwolotsa yolodani bwinobwino

[00:01:57] Nanga lero bwanji

[00:02:01] Kabwino konse upange ulalike utakwera chulu

[00:02:10] Namalenga sakondwa nazo

[00:02:13] Mphoto yako

[00:02:15] Udzalandiliratu

[00:02:18] Wanyoza mtundu wanga

[00:02:23] Iwe walakwa walakwa

[00:02:27] Waphetsa mtundu wanga

[00:02:31] Ndati walakwa

[00:02:32] Ndati walakwa

[00:02:35] Alikuti yosuayo

[00:02:39] Adzabwera liti

[00:02:40] Tifuna chipulumutso

[00:02:43] Sitifuna mose wina

[00:02:47] Wankhambakamwa

[00:02:49] Wodzatisocheretsa

[00:02:52] Alikuti yosuayo

[00:02:56] Adzabwera liti

[00:02:58] Tifuna chipulumutso

[00:03:01] Sitifuna mose wina

[00:03:04] Wankhambakamwa

[00:03:06] Wodzatisocheretsa

[00:03:09] Alikuti yosuayo

[00:03:13] Adzabwera liti

[00:03:15] Tifuna chipulumutso

[00:03:18] Sitifuna mose wina

[00:03:22] Wankhambakamwa

[00:03:24] Wodzatisocheretsa

您可能还喜欢歌手The Very Best的歌曲: